Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #69
Hymn 69 Tidzakhalitsa Pa Kasupe
[V1]
WE’LL TARRY BY THE LIVING WATERS 1. Tidzakhalitsa pa kasupe, Wa madzi akewo.
Kumene Yesu adikira, Kupatsa moyowo.
WE’LL TARRY BY THE LIVING WATERS 1. Tidzakhalitsa pa kasupe, Wa madzi akewo.
Kumene Yesu adikira, Kupatsa moyowo.
[C]
Tidzakhalitsa pa kasupe (wathu),
’Dzakhalitsa pa kasupe (wathu),
’Dzakhalitsa pa kasupe (wathu).
Pali madzi a moyo.
2. Tikatopatu ndi ulendo, Tidzapumulatu,
Pa mtsinje wopambana yonse, Wokondwakondwatu.
3. Idzani nonsenu kwa Khristu, Mudzamwe madziwo,
Adzatimwetsa kwa ulere, Kasupe wakeyo.