Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #71
Hymn 71 Kodi Dzina Langa Lalembedwamo?
[V1]
IS MY NAME WRITTEN THERE? 1. Mbuye sindisamala kukhala wachuma;
Ndifuna kukalowa m’dziko la kumwamba;
M’bukhu lokometsetsa la ufumu wanu,
Kodi lalembedwamo Mbuye dzina langa.
IS MY NAME WRITTEN THERE? 1. Mbuye sindisamala kukhala wachuma;
Ndifuna kukalowa m’dziko la kumwamba;
M’bukhu lokometsetsa la ufumu wanu,
Kodi lalembedwamo Mbuye dzina langa.
[C]
Kodi dzina langa, Lalembedwa m’mwamba?
M’bukhu la ufumuwo, Kodi lalembedwa?
2. Machimo anga alipo ambiri-mbiri,
Koma mwazi wa Mpulumutsi wandikwana;
Chifukwa lonjezano lanu lilipobe,
Ngakhale afiire, ndidzawayeretsa.
3. Ku mzinda wokoma wa malo owala’wo
Ndi anthu ovala za ulemelerozo;
Kumene choipa sichidzaonongako,
Kodi dzina langali lilipo m’bukhumo?
Kodi dzina langa, Lalembedwa m’mwamba?
M’bukhu la ufumuwo, Kodi lalembedwa?
2. Machimo anga alipo ambiri-mbiri,
Koma mwazi wa Mpulumutsi wandikwana;
Chifukwa lonjezano lanu lilipobe,
Ngakhale afiire, ndidzawayeretsa.
3. Ku mzinda wokoma wa malo owala’wo
Ndi anthu ovala za ulemelerozo;
Kumene choipa sichidzaonongako,
Kodi dzina langali lilipo m’bukhumo?