Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #47

Hymn 47 Ndaimirira pa Gombe

[V1]
ON JORDAN’S STORMY BANKS1. Ndaimirira pa gombe, Ndiyang’anitsitsa,
Ku Kanani wabwinoyo, Komwe ndidzalowa.

[C]

Tidzapumula mdziko lokondwa (lokondwa),
Kuoloka pa gombe lija (lowala),
Tidzayimba nyimbo ya Mose,
Ndikukhala ndi Yesu nthawi zonse.

[V2]
Pa madambo akuluwo, ’Dzawala tsikulo,
Khristu adzalamulira, Nadzachotsa mdima.

[C]

Tidzapumula mdziko lokondwa (lokondwa),
Kuoloka pa gombe lija (lowala),
Tidzayimba nyimbo ya Mose,
Ndikukhala ndi Yesu nthawi zonse.

[V3]
Ndidzafika uko liti, Ndikudalitsidwa,
N’dzamona liti Atate, Kuti ndikapume?

[C]

Tidzapumula mdziko lokondwa (lokondwa),
Kuoloka pa gombe lija (lowala),
Tidzayimba nyimbo ya Mose,
Ndikukhala ndi Yesu nthawi zonse.

[V4]
Moyo wanga ukondwera, Kusiya dzikoli;
Nkana namondwe aombe, Sindiopa konse.

[C]

Tidzapumula mdziko lokondwa (lokondwa),
Kuoloka pa gombe lija (lowala),
Tidzayimba nyimbo ya Mose,
Ndikukhala ndi Yesu nthawi zonse.

47. Ndaimirira pa Gombe

Link copied to clipboard successfully!