Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #48
Hymn 48 Chimwemwe Posachedwa
[V1]
Chimwemwe podzatha ntchitoyi, Podzasonkhana okunkha,
Alikudza ndi zipatso, Ku Yerusalemuko.
Chimwemwe podzatha ntchitoyi, Podzasonkhana okunkha,
Alikudza ndi zipatso, Ku Yerusalemuko.
[C]
Kudzakhala chimwemwedi,
Chimwemwe cha nthawi zonse,
Chifukwa nthawi yafika,
Yosonkhana okunkha.
Kudzakhala chimwemwedi,
Chimwemwe cha nthawi zonse,
Chifukwa nthawi yafika,
Yosonkhana okunkha.
[V1]
(Bass and Tenor):
Chimwemwe posachedwa,
Chimwemwe cha muyaya,
Chifukwa nthawi yafika,
Yosonkhana okunkha.
(Bass and Tenor):
Chimwemwe posachedwa,
Chimwemwe cha muyaya,
Chifukwa nthawi yafika,
Yosonkhana okunkha.
[C]
Kudzakhala chimwemwedi,
Chimwemwe cha nthawi zonse,
Chifukwa nthawi yafika,
Yosonkhana okunkha.
Kudzakhala chimwemwedi,
Chimwemwe cha nthawi zonse,
Chifukwa nthawi yafika,
Yosonkhana okunkha.
[V2]
Tidzayimba nyimbo zabwino, Tidzayamika mokondwa,
Tidzatama Khristu Mfumu, Mu mzinda watsopano.
Tidzayimba nyimbo zabwino, Tidzayamika mokondwa,
Tidzatama Khristu Mfumu, Mu mzinda watsopano.
[C]
Kudzakhala chimwemwedi,
Chimwemwe cha nthawi zonse,
Chifukwa nthawi yafika,
Yosonkhana okunkha.
Kudzakhala chimwemwedi,
Chimwemwe cha nthawi zonse,
Chifukwa nthawi yafika,
Yosonkhana okunkha.
[V3]
Chimwemwe chitidikirako, Ku malo a chikhuduwo;
Yesu ali kuwakonza, Mu Mzinda watsopano.
Chimwemwe chitidikirako, Ku malo a chikhuduwo;
Yesu ali kuwakonza, Mu Mzinda watsopano.
[C]
Kudzakhala chimwemwedi,
Chimwemwe cha nthawi zonse,
Chifukwa nthawi yafika,
Yosonkhana okunkha.
Kudzakhala chimwemwedi,
Chimwemwe cha nthawi zonse,
Chifukwa nthawi yafika,
Yosonkhana okunkha.