Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #38

Hymn 38 Limbikani Mwa Mulungu

[V1]
FIRMLY STAND FOR GOD 1 Limbikani mwa Mlungu wanuyo,
Nkana m’dziko muli mavutowo;
Khristu ndiye thanthwe lolimbalo,
Ndi la mphamvu zonsezo.

[C]

Tilimbike kuima pa thanthwe lija,
Thanthwe ndilo Khristuyo;
Ngati tipiriratu tidzankako,
Kuli mpando wa Mlunguyo.

2 Limbikani ndi mtima woti nji,
Inde mwa chikhulupirirocho;
Kristu ndiye thanthwe la mphamvulo,
Agonjetsa tchimolo.

3 Limbikani mwa choonadicho,
Chikuthangatani koposatu;
Kristu ndiye thanthwe lopumamo,
Mmene vuto latha phe.

38. Limbikani Mwa Mulungu

Link copied to clipboard successfully!