Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #12
Hymn 12 Kasupe Ali Wodzaza
[V1]
THERE IS A FOUNTAIN 1. Kasupe ali wodzaza,
Ndi mwazi wa Yesu;
Omwe asamba mwa uyu
Ataya zoipa.
2. Woba wakufa napenya,
Kasupe nakondwa;
Ndi ine enso mwa uyu,
Ndisamba ndiyera.
3. Mwazi wa Yesu wokondwa,
Ukhala wamphamvu;
Kwa ana onse a Mlungu
Uchita kuombola.
4. Mmene ndapenya mwazi
wa Mabala Anuwo,
Kukonda kwanu nditama
Kwa kutha kwa moyo.
5. Ndikhulupirira kuti
Mwakakonza malo
Ndipo ndidzalowa ine
Ku moyo wosatha.
6. Kumwamba ndikayimbanso
Zamphamvu za Mlungu,
Zopulumutsa onsewa
Omvana ndi Yesu.
THERE IS A FOUNTAIN 1. Kasupe ali wodzaza,
Ndi mwazi wa Yesu;
Omwe asamba mwa uyu
Ataya zoipa.
2. Woba wakufa napenya,
Kasupe nakondwa;
Ndi ine enso mwa uyu,
Ndisamba ndiyera.
3. Mwazi wa Yesu wokondwa,
Ukhala wamphamvu;
Kwa ana onse a Mlungu
Uchita kuombola.
4. Mmene ndapenya mwazi
wa Mabala Anuwo,
Kukonda kwanu nditama
Kwa kutha kwa moyo.
5. Ndikhulupirira kuti
Mwakakonza malo
Ndipo ndidzalowa ine
Ku moyo wosatha.
6. Kumwamba ndikayimbanso
Zamphamvu za Mlungu,
Zopulumutsa onsewa
Omvana ndi Yesu.