Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #4
Hymn 4 Ali Kudza
[V1]
HE IS COMING 1 Timamva uthenga wabwinotu, M’mene tiri kunka kwathu;
Msanga Mpulumutsi adzabwera, Kukhala Mfumu yathu.

[C]
Ali kudza posacedwa, Inde ali kudza pa dzikoli;
Ndipo tidzapita tonse kumwamba, Pakubwera Yesuyo.
2 Manda a anthu oyera mtima, Adzatsegulidwa ndithu;
Ndipo onse ogonera m’mandamo, Adzakhalanso moyo.
3 Sitidzalekananso kwathu ko, Tidzayimba za chombolo;
Anthu a mitundu yonse adzadza, Kupembedza Mfumuyo.
4 Tidzayimba aleluya, Amen! Msanga tikasamalira;
Dikirani ndi kupemphera nonse, Tidzabvala korona.