Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #286
Hymn 286 Nditengeni
[V2]
Ndidzamva Aliluyayo Kwa khamu likuru;
Ndikayimba nao nyimbo, Ya oomboledwa.
Ndidzamva Aliluyayo Kwa khamu likuru;
Ndikayimba nao nyimbo, Ya oomboledwa.
[C]
Nditengeni tengeni, Ku Ziyoni
Ku mudzi wachikondiwo. Ku mudzi wa Yesu.
Nditengeni tengeni, Ku Ziyoni
Ku mudzi wachikondiwo. Ku mudzi wa Yesu.
[V3]
Ndidzakamwone Israel Ndi Yesu Kalonga,
Ndi mpando wa mfumu yanga Yemwe ’natilenga.

[V4]
Ndifuna ku Yerusalemu, Ku mudzi wa Mfumu,
Ndifuna n’kadye zipatso Zotipatsa moyo.