Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #280

Hymn 280 Mfumu Yathu

[V1]
OUR KING 1. Nyimbo zathu zokoma, Tadza nazo lero,
Kudzayamika Mbuye, Njira ndi moyowo

[C]

Tiyimbatu kutamanda Mfumu (Mfumu)
Tiyimbatu Ulemu kwa Mfumu.

2. Anakonda tiana pokhala pansiopo,
Ngakhale ali m’mwamba amatikondabe.

3. TIkonda kumyimbira, Ndi kumva za Iye
Pamene anakhala pa dziko kalelo

4. Mpulumutsi wodala, Tikugwadirani,
Kuti mutithandize kukhulupiranu.

280. Mfumu Yathu

Link copied to clipboard successfully!