Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #279
Hymn 279 Idzani Kuno Kwa Ine
[V1]
"COME UNTO ME" 1. Ha! Mtima wacisoni maso osaona,
Mungathebe kukondwera mwa Yesu, Mbuyathu
"COME UNTO ME" 1. Ha! Mtima wacisoni maso osaona,
Mungathebe kukondwera mwa Yesu, Mbuyathu
[C]
Idzani kwa Ine nonsenu
Inu akutodwa ndipo mudzapume
Senza goli langa, phunzira
Ndiri wofatsa mumtimamo,
Mudzapumula m’myoyo yanu
Bass, Tenor & Alto
’Dzanitu, ’dzani kuno ’dzanitu, nonsenu otodwa
Alto
Inu akutodwa ndipo mudzapume.
Bass & Tenor
’Dzanitu akutodwanu, mudzapumula.
Alto, Tenor & Bass
’Dzanitu, senza gori, ’Dzanitu, phunziratu,
Tenor & Bass
Ndi wofatsa mtimamo, Mudzapumula m’moyo wanu.
2. Cimwemwe ca m’dzikoli sicikwanitsa’fe,
Cikondi cikondwetsa, cikondi ca Yesu.
3. Cisomo copambana ca Yesu Kristuyo
Cidzakhululukira olapa onsewo
4. Mtendere ngati mtsinje, cikondi ndi nyimbo
Ndi gori lakufewa tipeza mwa Yesu.