Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #281

Hymn 281 Nyenyezi Yabwino

[V1]
A BEAUTIFUL STAR 1. Nyenyezi yabwino yowala ndi ulemerero wa m’mwamba
Kuwala kwace kotsogoza anzeru napeza mwana

[C]

Yowalayo, yowalayo, Nyenyezi yabwino m’phiri,
Yowalayo, yowalayo, Cipulumutso ca Mlungu.

2. Mau anawadziwitsadi nthawi yafika ya nyenyezi,
Anaitsata yowalayo – Ndi "Kristu nthanda ya m’mawa"

3. Nafe titsate monga iwo, Muni wa dziko wonenedwa’
Titsate monga iwo, Muni wa dziko wonenedwa;
Titsate mpaka tikafike, Ku Mpumula wa kumwamba.

281. Nyenyezi Yabwino

Link copied to clipboard successfully!