Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #267
Hymn 267 Fesa Mbeuu Za Cikondi
[V1]
SCATTER SEEDS OF KINDNESS 1. Tisonkhanitse zabwino, M’njira mwathu monsemo;
Tisunge tirigu yekha, Titaye zacabezo;
Tipeze zokondweretsa M’madalitso a lero,
Mwa cipiriro ticotse Minga yokhumudwitsa.
SCATTER SEEDS OF KINDNESS 1. Tisonkhanitse zabwino, M’njira mwathu monsemo;
Tisunge tirigu yekha, Titaye zacabezo;
Tipeze zokondweretsa M’madalitso a lero,
Mwa cipiriro ticotse Minga yokhumudwitsa.
[C]
Ufese zacifundo, Ufese zacifundo
Ufese zacifundo, Zomwe tidzakolola
2. Sitisamala maluwa Ndi mbalame poyimba,
Mpaka mbalame ndiponso maluwa zitacoka;
Dzuwa sitisamala Pa nthawi ya cilimwe,
Akafikanso mazizi Nthaawiyo tilifuna.
3. Mwana akacita ngozi Poswa cikho comwera
Kodi mukalipa ko’psa Poturutsa tsinyalo?
Mukudziwa kuti mawa Adzakhala wakufa,
Kodi pakukwiya naye Mupsa Mtima leroli?
4. Poganizira za m’mbuyo Za zomwe tinacita,
Za mauwo okalipa Okhumutsidwa ena,
Ndi nchito zosaganiza; Izi zitikumbutsa
Kufetsatu zacifundo zomwe tidzakolola.