Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #239

Hymn 239 Kodi Uli Kulemedwa?

[V1]
ART THOUGH WEARY? 1. Kodi uli kulemedwa ndi zoipazo?
Idza kuno ati Yesu, Pumako.

2. Ndikamzindikira n’inji Mbuye wangayo?
Ali ndi mabala m’manja mwacemo.

3. Kodi ali ndi cilemba m’mphumi mwacemo?
E! Cilembaco ca minga cirimo.

4. Ndikampeza ndikamtsata ninji pansi?
Masauko ndi misozi ziripo.

5. Ndikamfunafuna Iye ndipezenjiko?
Kumariza kwa cisoni conse.

6. Ndikampempha anditenge ati bwanji ko?
Ati Yesu "Idza msanga, idzatu."

7. Kukamtsata, kukampeza ndisaukanji?
Oyera, atumwi, ati idzani.

Amen.

239. Kodi Uli Kulemedwa?

Link copied to clipboard successfully!