Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #233

Hymn 233 Uzeni Nthano Yakale

[V1]
TELL ME THE OLD, OLD STORY 1. Uze nthano yakale, Ya za kumwambako,
Za Yesu wacifundo, Za Yesu wokonda;
Pang’ono pang’onotu, monga kwa kamwana,
Poti ndiri wotopa, wopanda thandizo.

[C]

Nthano yakale uze, Nthano yakale uze,
Nthano yakale uze, Ya Yesu wokonda.

2. Pang’ono ndi pang’ono, Motsimikizadi;
Pakuti ndaipadi, Yesu nandifera;
Nthano yonseyo uze, Musacite mphwayi,
M’nthawi yonse ya bvuto, Andisangalatsa.

3. Nenatu yomwe ija, Ukhala ndi mantha,
Kuti dziko loipa, Ndilikondetsetsa;
Ulemu wa dzikowu Uyamba m’moyomu,
Uze nthano yakale; Yesu akuciza.

233. Uzeni Nthano Yakale

Link copied to clipboard successfully!