Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #234

Hymn 234 Yesu Nyali Ya Dziko

[V1]
JESUS THE LIGHT OF THE WORD 1. Ha! Nayimba angelo, Yesu nyali ya dziko;
Mwana wabadwa Mfumu, Yesu nyali ya dziko.

[C]

Yenda m’kuunika kwabwiniko,
Idza kumene kuli cifuno,
Kuwala kwa msana ndi usiku;
Yesu, nyali ya dziko.

2. Mapfukonu kondwani, Yesu nyali ya dziko;
Kondwani ndi a m’mwamba, Yesu nyali ya dziko.

3. M’mwamba amlekeza, Yesu nyali ya dziko;
Yesu Mbuye wosatha, Yesu nyali ya dziko.

4. Mfumu ya mtenderedi, Yesu nyali ya dziko;
Dzuwa la cilungamo, Yesu nyali ya dziko.

234. Yesu Nyali Ya Dziko

Link copied to clipboard successfully!