Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #229
Hymn 229 Wa Yesuyo Ndani?
[V1]
WHO IS ON THE LORD’S SIDE 1. Wa Yesuyo ndani? Ngoona;
Mbali ndi ziwiri; Usankhe
WHO IS ON THE LORD’S SIDE 1. Wa Yesuyo ndani? Ngoona;
Mbali ndi ziwiri; Usankhe
[C]
Sankha, sankha (Wa Yesuyo ndani? Wa Yesuyo ndani?)
Yabwino, yoipa? Usankhe
Sankha, sankha,
Yabwino, yoipa? Usankhe.
2. Ambiri asankha Yoipa;
Yosalimba ndi ya mabodza.
3. Gwirizana naye Ambuye,
Ndiyo mbali yokha yolimba.
Sankha, sankha (Wa Yesuyo ndani? Wa Yesuyo ndani?)
Yabwino, yoipa? Usankhe
Sankha, sankha,
Yabwino, yoipa? Usankhe.
2. Ambiri asankha Yoipa;
Yosalimba ndi ya mabodza.
3. Gwirizana naye Ambuye,
Ndiyo mbali yokha yolimba.