Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #230

Hymn 230 Ndine Njira

[V1]
I AM THE WAY 1. Monga nkhosa zotayika, Zomwazika konse;
Zasiya moyo, mtendere, Njira yandisowa?

[C]
(Sop. & alto):
Ndine njira, co’nadi, moyo
Sungafike Atate koma mwa Ine,
Ndine njira, co’nadi, moyo,
Sungafike Atate komwa mwa Ine

(Bass and Tenor):
Ndine njira, ndine njira, ndine njira co’nadi, moo
Sungafike Atate koma mwa ine,
Ndine njira, ndine njira, ndine njira co’nadi, moyo
Sungafike Atate koma mwa ine.

2. Nkhawa zandisokoneza, Mulungu ndifuna;
Manena-nena ngambiri, Ndingagwire ziti?

3. Kwa Kristu, njira, co’nadi Ndi moyo ndibweranso;
Adzandifitsa kwa Tate, Kumalo kosatha.

230. Ndine Njira

Link copied to clipboard successfully!