Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #216
Hymn 216 Sindiri Ndekha
[V1]
NEVER ALONE 1. Ndekha? Bi, sindiri ndekha Yesu ngwanga;
Amandisangalatsa; ali pafupipa,
Ulibe bwenzi ko, Ndiri naye Yesu;
Ndimasinthasinthadi, Iye sasinthatu.
NEVER ALONE 1. Ndekha? Bi, sindiri ndekha Yesu ngwanga;
Amandisangalatsa; ali pafupipa,
Ulibe bwenzi ko, Ndiri naye Yesu;
Ndimasinthasinthadi, Iye sasinthatu.
[C]
Sindiri ndekha, sindiri ndekha;
Anapangana nane kuti sadzandisiya ndekha.
2. Kutopa? Nditoperenji, Yesu ngwanga;
Ndatsamira pa Iye, Ndiri kupumula,
Wosowawe; Inde ndatsamira zedi,
Pa dzanja lace Yesu phe Andisamalira.
3. Kulindira? Inde, kulindira;
Kaya acedweranji Ambuye kubwera,
Ndiye ukukondwa? Inde, kukondwadi;
Ndikondwa ndi maziko ndiye Ambuyanga.
Sindiri ndekha, sindiri ndekha;
Anapangana nane kuti sadzandisiya ndekha.
2. Kutopa? Nditoperenji, Yesu ngwanga;
Ndatsamira pa Iye, Ndiri kupumula,
Wosowawe; Inde ndatsamira zedi,
Pa dzanja lace Yesu phe Andisamalira.
3. Kulindira? Inde, kulindira;
Kaya acedweranji Ambuye kubwera,
Ndiye ukukondwa? Inde, kukondwadi;
Ndikondwa ndi maziko ndiye Ambuyanga.