Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #215

Hymn 215 Linda Usadandaule

[V1]
WAIT AND MURMUR NOT 1. Kwathu kosasinthikako, Ndi masautso kulibe;
Inde kwathu kowalako, Kodi sudzapumulako?

[C]

Linda, usadandauletu, Linda usadandauletu;
Linda, Linda, Usadandauletu.

2. Walemedwa ndi katundu, Wa zinthu za dziko lino,
Tsiku lopuma lidzadza( fatsa usadandaule.

3. M’njira muli minga kodi, Iye anabvala minga;
Wapeza cisoni kodi, Iye cinamgwera kale.

4. Gwira ntchito upirire, Ngakhale umanyozeka;
Tsiku lopuma lifika, Linda usadandaule.

215. Linda Usadandaule

Link copied to clipboard successfully!