Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #201
Hymn 201 Anandibvuula
[V1]
HE BROUGHT ME OUT 1. Mtima wanga unaopa Yehova
Ntakanikizidwa pansi ndi cimo;
Ndamulirira Ambye m’thopemo,
Anandibvuulamo mwa cifundo.
HE BROUGHT ME OUT 1. Mtima wanga unaopa Yehova
Ntakanikizidwa pansi ndi cimo;
Ndamulirira Ambye m’thopemo,
Anandibvuulamo mwa cifundo.
[C]
Anandibuula m’matope,
Nandikhazikitsa pa thanthwe;
Moyo wanga lero uyimba,
Matamando Haleluya
2. Wandikhazika pa thanthwe lolimba,
Ndakhazikitsidwa sindicokapo;
Pano palibe coopsya ndakhala,
Cisomo cidzandibveka korona.
3. Wandipatsa nyimbo ya mayamiko,
Msana ndi usiku ndidzayimba;
Mtimawu useka ndi ufulu,
Ndikutamandani Mombolo wanga.
4. Ndidzayimba nsisi mwandicitira,
Ndzalimbika mpaka onse amdziwe;
Cipulumutso ndzayimba konseko.
Kuti ambiri amvere Mulungu
Anandibuula m’matope,
Nandikhazikitsa pa thanthwe;
Moyo wanga lero uyimba,
Matamando Haleluya
2. Wandikhazika pa thanthwe lolimba,
Ndakhazikitsidwa sindicokapo;
Pano palibe coopsya ndakhala,
Cisomo cidzandibveka korona.
3. Wandipatsa nyimbo ya mayamiko,
Msana ndi usiku ndidzayimba;
Mtimawu useka ndi ufulu,
Ndikutamandani Mombolo wanga.
4. Ndidzayimba nsisi mwandicitira,
Ndzalimbika mpaka onse amdziwe;
Cipulumutso ndzayimba konseko.
Kuti ambiri amvere Mulungu