Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #99
Hymn 99 Pokumbukira Mtandawo
[V1]
Pokumbukira mtandawo Umene Mbuye nafapo,
Zokoma za pa dzikoli Sizinga kanthu konse bi.

[V2]
Onani mutu, manjanso, Mapazi ndi mu nthitimo.
E! panalibe winayo Wondivalira mingayo.

[V3]
Chinkana ndinachimwatu, Anakhulukira ’ne.
Ndisadzitame ndekhai, Nditame mtanda wakewo.

[V4]
Chinkana ndipereketu, Ee! chuma chonse m’dzikomo,
Sizingakwane konsei, Ndingopereka mtimanga.