Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #86
Hymn 86 Gwadwani Pa Maso Pa Mfumu
[V1]
Gwadani pa maso a Mfumuyo,
Yimbani chikondi cha Mbuyeyo;
Iyeyo n’chikopa, mtetezi wathu,
Amene akhala kumwamba komwe.
Gwadani pa maso a Mfumuyo,
Yimbani chikondi cha Mbuyeyo;
Iyeyo n’chikopa, mtetezi wathu,
Amene akhala kumwamba komwe.
[V2]
Yimbani za mphamvu ya Mlunguyo,
Ndi za nsisi zake kwa ifetu;
Amakhala m’mphezi ndi m’bingu momwe,
Ambuye avala zoyeratu mbu.
Yimbani za mphamvu ya Mlunguyo,
Ndi za nsisi zake kwa ifetu;
Amakhala m’mphezi ndi m’bingu momwe,
Ambuye avala zoyeratu mbu.
[V3]
Chikondi chake ndi chakuyatu,
Chimaonekera mu dzuwalo;
M’mitsinje, m’mapiri, m’madambo momwe,
Mu mvula, mu mame, ndi m’zina zonse.
Chikondi chake ndi chakuyatu,
Chimaonekera mu dzuwalo;
M’mitsinje, m’mapiri, m’madambo momwe,
Mu mvula, mu mame, ndi m’zina zonse.
[V4]
Ndifetu opanda mphamvu konse,
Tithemba pa Inu, Mbuyathuyo;
Mwa nsisi za inu mtisunge ife;
Mtetezi ndi Mlengi ndi Bwenzi lathu.
Ndifetu opanda mphamvu konse,
Tithemba pa Inu, Mbuyathuyo;
Mwa nsisi za inu mtisunge ife;
Mtetezi ndi Mlengi ndi Bwenzi lathu.