Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #82

Hymn 82 M’mawa

[V1]
M’dzamva mau anga m’mawa
Mbuye popemphera;
Ndidzayang’ana kwa Inu
M’mene ndipemphera.

[V2]
Mzimu anditsogolere
M’njira zolungama!
Andisonyeze njira za
Ntchito zanga zonse.

[V3]
Anthu okonda dzinalo
Adzakwanitsidwa;
Mulungu adzawaphimba
Ndi chikopa chake.

82. M’mawa

Link copied to clipboard successfully!