Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #81

Hymn 81 Gwira Zinchito Zake

[V1]
Gwira zintchito zake, Mdima ukudzatu,
Yamba mmamawa ndithu, Kuli kuchatu.
Gwiranso msana monse, Mpaka madzulowo.
Gwira, usiku udza, Posachedwatu.

[V2]
Gwira zintchito zake, Mdima ukudzatu,
Gwira masana onse, Kusanadei.
Udzapumula bwino, Potha zintchitozo,
Gwira, usiku udza, posachedwatu.

[V3]
Mkhristu gwiratu ntchito, Mdima ukudzatu,
Dzuwa lapita kale, Msanga kuda bi!
Gwira madzulodzulo, Usanagonetu,
Msanga zintchito zonse Tere zithatu.

81. Gwira Zinchito Zake

Link copied to clipboard successfully!