Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #83
Hymn 83 Anthu Ambiri Ayimba
[V1]
Anthu ambiri ayimba, Lodala dzina la Mbuye!
Ulemelero kwa Mlungu, Lodala dzina la Mbuye.

[C]
Dzina lodala, dzina lodala, dzina la Ambuye Yesu.

[V2]
Dzinali lichotsa mantha, Lodala dzina la Mbuye!
Lili nyimbo ya ochimwa, Lodala dzina la Mbuye.

[V3]
Athyola mphamvu ya tchimo, Lodala dzina la Mbuye!
Mwazi wake utitsuka, Lodala dzina la Mbuye.