Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #50
Hymn 50 Bwinoli Tipita
[V1]
Kuli dziko labwino m’mwamba
Lakuwala koposa dzuwa,
Ndi Atate akonza malo,
Pokhalira ife komweko.
Kuli dziko labwino m’mwamba
Lakuwala koposa dzuwa,
Ndi Atate akonza malo,
Pokhalira ife komweko.
[C]
Bwinoli tipita,
Tikomana ku dziko lija (lijalo).
Bwinoli tipita,
Tikomana ku dziko lija (lijalo).
[V2]
Tidzayimba komweko nyimbo,
Za abwino omvera Yesu,
Sitidzamvatu zisoninso,
Tidzakondwa masiku onse.
Tidzayimba komweko nyimbo,
Za abwino omvera Yesu,
Sitidzamvatu zisoninso,
Tidzakondwa masiku onse.
[C]
Bwinoli tipita,
Tikomana ku dziko lija (lijalo).
Bwinoli tipita,
Tikomana ku dziko lija (lijalo).
[V3]
Tidzatama Atate wathu,
Kuti iye ’napatsa Yesu,
Kuchotsera zochimwa zonse,
Ndi kutidalitsira ife.
Tidzatama Atate wathu,
Kuti iye ’napatsa Yesu,
Kuchotsera zochimwa zonse,
Ndi kutidalitsira ife.
[C]
Bwinoli tipita,
Tikomana ku dziko lija (lijalo).
Bwinoli tipita,
Tikomana ku dziko lija (lijalo).