Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #49
Hymn 49 Ganizo Lokoma
[V1]
ONE SWEETLY SOLEMN THOUGHT1. Ganizo lokoma, Limadza m’mtimamu;
Ndili pafupi ndi kwathu, Koposa kalelo.
ONE SWEETLY SOLEMN THOUGHT1. Ganizo lokoma, Limadza m’mtimamu;
Ndili pafupi ndi kwathu, Koposa kalelo.
[C]
Pafupitu, Ndi kwathuko;
Ndili pafupi ndi kwathu, Koposa kalelo.
Pafupitu, Ndi kwathuko;
Ndili pafupi ndi kwathu, Koposa kalelo.
[V2]
Kufupi ndi Tate, Komwe kuli malo;
Ku mpando wa Yesu Mbuye Ku nyanja yoyera.
Kufupi ndi Tate, Komwe kuli malo;
Ku mpando wa Yesu Mbuye Ku nyanja yoyera.
[C]
Pafupitu, Ndi kwathuko;
Ndili pafupi ndi kwathu, Koposa kalelo.
Pafupitu, Ndi kwathuko;
Ndili pafupi ndi kwathu, Koposa kalelo.
[V3]
Ndili kupitatu, Nditula katundu;
Ndisiya mtanda wangawo, Kuvala korona.
Ndili kupitatu, Nditula katundu;
Ndisiya mtanda wangawo, Kuvala korona.
[C]
Pafupitu, Ndi kwathuko;
Ndili pafupi ndi kwathu, Koposa kalelo.
Pafupitu, Ndi kwathuko;
Ndili pafupi ndi kwathu, Koposa kalelo.