Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #51

Hymn 51 Mutibatizenso

[V1]
Mutibatize ndi mphamvu yanu,
Mutitsitsimutse mwa nsoni zanu.

[C]
(wotsiriza):
Tigwadira Inu Mwana wa nkhosa,
Tikupembedzani kosatha, Amen.

[V2]
Osayenera ndi ochimwa’fe
Mutitsuke ife m’zoipa zathu.

[C]
(wotsiriza):
Tigwadira Inu Mwana wa nkhosa,
Tikupembedzani kosatha, Amen.

[V3]
Tifuna nkhunda ya m’mwamba idze
Idzatidalitse mwa nsoni zanu.

[C]
(wotsiriza):
Tigwadira Inu Mwana wa nkhosa,
Tikupembedzani kosatha, Amen.

[V4]
Imvani mau ochoka m’mwamba,
Ndiwe mwana wanga wokondedwayo.

[C]
(wotsiriza):
Tigwadira Inu Mwana wa nkhosa,
Tikupembedzani kosatha, Amen.

51. Mutibatizenso

Link copied to clipboard successfully!