Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #44
Hymn 44 Ndidzamdziwa Mombolo Wanga
[V1]
WHEN MY LIFE-WORK IS ENDED 1. Pamene nditatha zintchito zanga zonsezo,
Nditaoloka pa tsidya la nyanja;
Chakufachi chikadzavalatu chosafanso;
Pompo ndidzamdziwa Mombolo wanga.

[C]
Ndidzamdziwa, Ndidzamdziwa, Podzaima pa mbali pakepo,
Ndidzamdziwa, ndidzamdziwa, Ndi misomali m’manja mwake.

[V2]
Moyo wanga udzakondwera pakumuona,
Ndi kuona nkhope yake yowala;
Ndidzamyamika Iye ndi mtima wanga wonse,
Malo adandikonzera kumwamba.

[V3]
Ee! ndidzakondwa pakuona okondedwawo
Omwe ndalekana nawo m’dzikoli;
Koma n’dzayamba ndaonana naye Yesuyo,
Wokondedwa wanga wopambanayo.

[V4]
Kupyolera pa zipata kunka ku mzindawo,
Iye adzanditsogolera ine,
Nyimbo ya nthawi zonse ndidzayimba mokondwa;
Nditamuona Mpulumutsi wanga.