Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #27

Hymn 27 M’titsitsimutse

[V1]
Tiyamika’Nu Mulungu wokonda,
Chifukwa cha Yesu Mwana wanuyo.

[C]
Haleluya, tidzamtama, Haleluya, Amen;
Haleluya timpembedza, Mulungu wathu.

[V2]
Tiyamikira, Mulungu wamphamvu;
Chifukwa cha Mzimu wanu Woyera.

[C]
Haleluya, tidzamtama, Haleluya, Amen;
Haleluya timpembedza, Mulungu wathu.

[V3]
Tiyamikira, Mwana wa Nkhosayo,
Yemwe anafera zoipa zathu.

[C]
Haleluya, tidzamtama, Haleluya, Amen;
Haleluya timpembedza, Mulungu wathu.

[V4]
Tiyamika’Nu, Mlungu wa chisomo,
Munatigula ndi mwazi wanuwo.

[C]
Haleluya, tidzamtama, Haleluya, Amen;
Haleluya timpembedza, Mulungu wathu.

[V5]
M’titsitsimutse, Ndi chikondi chanu,
M’tiyatse ndi moto wa Mzimu wanu.

[C]
Haleluya, tidzamtama, Haleluya, Amen;
Haleluya timpembedza, Mulungu wathu.

27. M’titsitsimutse

Link copied to clipboard successfully!