Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #23

Hymn 23 Mundifungatire Ine

[V1]
HOVER O’ER ME HOLY SPIRIT 1. Mundifungatire ine, Mzimu wakuyera ’Nu,
Munditsuke mtima wanga, Inde, Mudze leroli.

[C]

Mudzetu, mudzetu, Mzimu wakuyera mbu.
Munditsuke mtima wanga, Inde, mudze leroli.

[V2]
Mzimu, mundidzaze ine, Ndisowatu nzeruzo.
Ndisowanso inu, Mbuye, Mundidzaze mtimanga.

[C]

Mudzetu, mudzetu, Mzimu wakuyera mbu.
Munditsuke mtima wanga, Inde, mudze leroli.

[V3]
Ine ndine wolefuka, Ndikugwadiranitu.
Mzimu Inu mundidzaze Ndi chikondi Chanucho.

[C]

Mudzetu, mudzetu, Mzimu wakuyera mbu.
Munditsuke mtima wanga, Inde, mudze leroli.

[V4]
Dalitseni ine, Mzimu, Sambitseni mtimanga.
Inu, Msangalatsi wanga, Mudze, inde leroli.

[C]

Mudzetu, mudzetu, Mzimu wakuyera mbu.
Munditsuke mtima wanga, Inde, mudze leroli.

23. Mundifungatire Ine

Link copied to clipboard successfully!