Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #22
Hymn 22 Inenso
[V1]
LORD, I HEAR1. Mbuye ndamva muchitira, Anthu ena zabwino;
Muli kuwadalitsira, Mudalitse inenso.
LORD, I HEAR1. Mbuye ndamva muchitira, Anthu ena zabwino;
Muli kuwadalitsira, Mudalitse inenso.
[C]
Inenso, inenso, Mudalitse inenso.
Inenso, inenso, Mudalitse inenso.
[V2]
Tate m’sandipitirire, Ndimaipa mtimamo;
Ndiyenera imfa, koma Chitireni chifundo.
Tate m’sandipitirire, Ndimaipa mtimamo;
Ndiyenera imfa, koma Chitireni chifundo.
[C]
Inenso, inenso, Mudalitse inenso.
Inenso, inenso, Mudalitse inenso.
[V3]
Ndinagona mwa zoipa, Ndinakunyozanitu,
Dziko lino ndinakonda, Mundikhululukire.
Ndinagona mwa zoipa, Ndinakunyozanitu,
Dziko lino ndinakonda, Mundikhululukire.
[C]
Inenso, inenso, Mudalitse inenso.
Inenso, inenso, Mudalitse inenso.
[V4]
Mzimu m’sandipitirire, Mupenyetsa akhungu;
Munapatsa ena mphamvu, Mpatse mphamvu inenso.
Mzimu m’sandipitirire, Mupenyetsa akhungu;
Munapatsa ena mphamvu, Mpatse mphamvu inenso.
[C]
Inenso, inenso, Mudalitse inenso.
Inenso, inenso, Mudalitse inenso.