Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #24

Hymn 24 Ndifuna Yesuyo

[V1]
Ndifuna Yesuyo, Ambuyanga,
M’mtendere ndinkemo, Mwa Iyeyu.

[C]
Ndifuna Inu, Yesu, Nthawiyi ndifuna,
Kwa Yesuyo, Mbuyanga, Ndifunako.

[V2]
Ndifuna Yesuyo, Movutamu,
Ndipulumukemo Mwa Iyeyu.

[C]
Ndifuna Inu, Yesu, Nthawiyi ndifuna,
Kwa Yesuyo, Mbuyanga, Ndifunako.

[V3]
Ndifuna Yesuyo, Mokondwa ndi
Mowawa, adzemo Ndi moyodi.

[C]
Ndifuna Inu, Yesu, Nthawiyi ndifuna,
Kwa Yesuyo, Mbuyanga, Ndifunako.

[V4]
Ndifuna yesuyo, Ndichite ’ne
Zofuna zakezo, Ndidzazebe.

[C]
Ndifuna Inu, Yesu, Nthawiyi ndifuna,
Kwa Yesuyo, Mbuyanga, Ndifunako.

[V5]
Ndifuna Yesuyo Woyeratu,
Ndikhale wakeyo, Wa Iyeyu.

[C]
Ndifuna Inu, Yesu, Nthawiyi ndifuna,
Kwa Yesuyo, Mbuyanga, Ndifunako.

24. Ndifuna Yesuyo

Link copied to clipboard successfully!