Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #20
Hymn 20 Moyo Wanga Dzuka
[V1]
Moyo wanga dzuka, limba Thamanga ndi mphamvu;
Korona wosatha ali, Kulindira iwe.
Moyo wanga dzuka, limba Thamanga ndi mphamvu;
Korona wosatha ali, Kulindira iwe.
[V2]
Mau a Mulungu wako, Akuitana’we;
Dzanja lake likufupa, Ngati ufunitsa.
Mau a Mulungu wako, Akuitana’we;
Dzanja lake likufupa, Ngati ufunitsa.
[V3]
Mtambo wa mboni wozinga, Uyang’anira’we;
Iwala zonse za m’mbuyo, Pitabe m’tsogolo.
Mtambo wa mboni wozinga, Uyang’anira’we;
Iwala zonse za m’mbuyo, Pitabe m’tsogolo.
[V4]
Mpulumutsi tikokeni, Tiyambe liwiro;
Tidze pa mapazi anu, Kutula katundu.
Mpulumutsi tikokeni, Tiyambe liwiro;
Tidze pa mapazi anu, Kutula katundu.