Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #315
Hymn 315 Mmene Ine Ndiri Mwana
[V1]
I WILL EARLY SEEK THE SAVIOUR 1. Mmene ine ndiri mwana Ndzaphunzira zacezo;
Ndidzamtsata Yesu yekha, M’njira ya mabvutoyo
I WILL EARLY SEEK THE SAVIOUR 1. Mmene ine ndiri mwana Ndzaphunzira zacezo;
Ndidzamtsata Yesu yekha, M’njira ya mabvutoyo
[C]
Inde, Yesu andikonda, Ine ndikudziwadi
Kuti Yesu andikonda, Nandiferakelelo.
2. Ndzanka komwe andiuza Sinnacepe konse bi,
Pakuyenda m’njira yace, Pena mcifuniro ’ce.
3. Iye Mpopulumukira Kwa zoipa zathuzo,
Iye anditsogolera, Ndikalowe mmambamo.