Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #316

Hymn 316 Tiri Otumika

[V1]
MISSIONARY VOLUNTEERS 1. Tiri otumika A Yesu Kristuyo,
Tapangana tidzagwira ntchito ya Ambuye

[C]

Ndifetu! Ndifetu! Otumikawo
Ndifetu! Ndifetu! A Ambuyeyo
Tsiku liri lonseli, caka ncakanso,
Tidzagwira ntchito yace, otumika ’fe.

2. Anyamata onsewo, atsikananso,
Tisatsate dziko lino, koma Yesu mwini

3. Akufunatu onsewo m’nchito yaceyo,
Tionetse za cikondi ndi cisomo cace.

4. Mpaka Yesu adzanso, tidzagwirabe
Tifuna kudzamva mau, "Munacita bwino".

316. Tiri Otumika

Link copied to clipboard successfully!