Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #311
Hymn 311 E, Mzimuu Wa Mulungu ’Nu
[V1]
O SPIRIT OF THE LIVING GOD 1. E, Mzimu wa Mulungu, ’Nu, Mukhale m’mtimanga;
Ndi zangazo ndipatsatu Kwa Inu, Mbuyanga

[C]
Mdzaze, mdzaze ’ne, Mdzaze Mzimu Woyera ’Nu,
Mdzaze, mdzaze ’ne, Wanu ndikhaletu.
2. Ndifunatu kucitadi Kufuna kwanuko;
Sin’funa kanthu kena bi, Mndidzaze, mtimamo,
3. Ndilibe kanthu kabwino, Kopatsa Inuyo;
Mutsuke Mtima wangawo, Ndi mwazi wanuwo.