Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #310
Hymn 310 Ndifuna Kukhala Ndi Yesu
[V1]
I WANT TO LIVE CLOSER TO JESUS 1. Ndifuna kukhala ndi Yesu, Kuyang’ana nkhope yace,
Adzaze mtimanga cisomo cace, Ndifuna kukhala naye.

[C]
Khala pafupi, mfupi nd Yesu, Pa mbali ya Iyeyo;
Kuyang’ana pa nkhope yabwinoyo, Ndifuna kukhala naye.
2. Ndifuna kukhala ndi Yesu, Kumtsata pafupifupi
Ndi kuti ndimvetse polankhula ’Ye, ponena lonjezo lace.
3. Ndifuna kukhala ndi Yesu, Pafupi masiku onse
Pogwiratu dzanja la mphamvu yace, Nkalowa m’ufumu wace.