Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #312
Hymn 312 Taitanidwa Kubatizidwa
[V1]
CALLED TO BE BAPTIZED 1. Tainanidwatu, Kuli mtsinje Yordano;
Ife tinamvadi Mau mcipululumo
CALLED TO BE BAPTIZED 1. Tainanidwatu, Kuli mtsinje Yordano;
Ife tinamvadi Mau mcipululumo
[C]
Ife tafikadi Kubatizidwamo,
Kuti titsukidwa Mphululupulu zathuzo.
2. Tamva Uthangawo, Wa cikondi caceco
Lapani m’mtimamo, Yesu ali kudzanso
3. Yesu anenanso, Yemwe akhulupira,
Nabatizidwa ’ye, Adzapulumukadi.
4. Tiyamikiratu Nsisi zace Yesuyo;
Watiturusadi Mdima wa zoipazo.
Ife tafikadi Kubatizidwamo,
Kuti titsukidwa Mphululupulu zathuzo.
2. Tamva Uthangawo, Wa cikondi caceco
Lapani m’mtimamo, Yesu ali kudzanso
3. Yesu anenanso, Yemwe akhulupira,
Nabatizidwa ’ye, Adzapulumukadi.
4. Tiyamikiratu Nsisi zace Yesuyo;
Watiturusadi Mdima wa zoipazo.