Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #256

Hymn 256 Mulungu Munathangata

[V1]
OUR HELP IN ACES PAST 1. Mulungu munathangata, Mudzathangathabe;
Woticinjiriza mz’opsa, Kwanu mutifitse!

2. Mwa mthunzi wa mpando wanu, Ndimo tibisala
Dzanja lanu liposadi, Tiri mosunguka.

3. Dziko linakhazikidwa Mapiri naima,
Mulungu wosamariza, Zako zosathera

4. Zaka ngati usiku, M’mawa kusanace.

256. Mulungu Munathangata

Link copied to clipboard successfully!