Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #255

Hymn 255 Ndikusowani Yesu

[V1]
I NEED THEE PRECIOUS JESUS 1. Ndikusowani Yesu, Ndiri waumphawi;
Mlendo wopanda malo, Za dziko ndilibe.
A Yesu Mudnikonde, Mundicingamire,
Ndikunditsogolera, Mphamvu yanga ndinu.

2. Ndisowa Mtima wanu, Kudziwa nkhawazo,
Ndi mayesero anga, Ndi zacisonizo.
Nsowa Mzimu Woyera, Womandiphunzitsa,
Kundiuzane Yesu, Ndi Mwana wa nkhosa.

3. Ndikusowani Yesu, Ndionane nanu,
Mu uta-wa-lezamo, Pa cimpando canu.
Ndi ogulidwa m’mazi, Ndikakondwerere
Nyimbo zosadukiza, Ndikumpenyetsetsa.

Amen.

255. Ndikusowani Yesu

Link copied to clipboard successfully!