Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #220
Hymn 220 Kwathu
[V1]
THE HOMELAND 1. Ndilakalaka kwathu! Dziko laufulu!
Kwathu kopanda mdima, Kulibe usiku;
Ndiri kulira kwathu, Mtima suli bwino;
Kulibe z owawa kwathu, Ndayandikirako;
Kulibe zowawa kwathu, Ndayandikirako.
2. Mbuyanga ali kwathu, Angelo abwino;
Kulibe chimo kwathu, Mayeso kulibe;
Nyimbozo za kwathuko Ndiri kuzimvatu
Ndikaganiza za kwathu Ndilira misozi
Ndikaganiza za kwathu Ndilira misozi
3. Anthu okhala kwathu Andikodolane,
Kopanda zacisoni Kwa okhala mommo;
Komomadi kwathuko! Kwa mtendere uko!
Kristu atifitsa kwathu Mwini wotikonda;
Kristu atifitsa kwathu Mwini wotikonda.
THE HOMELAND 1. Ndilakalaka kwathu! Dziko laufulu!
Kwathu kopanda mdima, Kulibe usiku;
Ndiri kulira kwathu, Mtima suli bwino;
Kulibe z owawa kwathu, Ndayandikirako;
Kulibe zowawa kwathu, Ndayandikirako.
2. Mbuyanga ali kwathu, Angelo abwino;
Kulibe chimo kwathu, Mayeso kulibe;
Nyimbozo za kwathuko Ndiri kuzimvatu
Ndikaganiza za kwathu Ndilira misozi
Ndikaganiza za kwathu Ndilira misozi
3. Anthu okhala kwathu Andikodolane,
Kopanda zacisoni Kwa okhala mommo;
Komomadi kwathuko! Kwa mtendere uko!
Kristu atifitsa kwathu Mwini wotikonda;
Kristu atifitsa kwathu Mwini wotikonda.