Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #193

Hymn 193 Kodi Ungakhale Moyo Wonga Wacewo?

[V1]
Kodi ungakhale moyo wonga Wakewo?
Kumayenda naye m’njira monsemo?
Ungamlole Iye kunyamula nkhawazo?
Mlole atsogole ’Ye.

[C]
Mwa mphamvu Yake udzakhalatu,
Wakumasuka, inde, m’mwazi ’ke.
Chikondi ’ke chidzaze mtimako,
Poyenda nawe zidamkonda ’Ye.

[V2]
Ungamlole kuti Iye amasule ’we?
Kuti umutsate poitana ’Ye?
Ungamlole kukutchinjiriza Mbuyeyo?
Mlole atsogole ’Ye.

[C]
Mwa mphamvu Yake udzakhalatu,
Wakumasuka, inde, m’mwazi ’ke.
Chikondi ’ke chidzaze mtimako,
Poyenda nawe zidamkonda ’Ye.

[V3]
Monga ukapeza malo mu ufumuwo?
Ungamyese akusamalire ’we?
Ungagwire ntchito Yake kopambanadi?
Mlole atsogole ’Ye.

[C]
Mwa mphamvu Yake udzakhalatu,
Wakumasuka, inde, m’mwazi ’ke.
Chikondi ’ke chidzaze mtimako,
Poyenda nawe zidamkonda ’Ye.

193. Kodi Ungakhale Moyo Wonga Wacewo?

Link copied to clipboard successfully!