Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #192

Hymn 192 Pa Mtanda Pomwe Naferapo

[V1]
Pa mtanda pomwe naferapo,
Pomwe ndalira ndi tchimolo,
Anandipaka ndi mwaziwo,
Tama dzinalo.

[C]
Tama dzinalo, Tama dzinalo,
Anandipaka ndi mwaziwo,
Tama dzinalo.

[V2]
Nandiwombola m’zoipazo,
Yesu akhala mu mtimanga,
Nandilandira pa mtandapo,
Tama dzinalo.

[C]
Tama dzinalo, Tama dzinalo,
Anandipaka ndi mwaziwo,
Tama dzinalo.

[V3]
Ndiye Kasupe Woyerayo!
Ndikondwa kuti ndasambamo,
Yesu watsukadi inenso,
Tama dzinalo.

[C]
Tama dzinalo, Tama dzinalo,
Anandipaka ndi mwaziwo,
Tama dzinalo.

[V4]
Idza kwa Yesu kasupeyo,
Igwa pa mapazi akewo,
Sambamo lero uyeretu,
Tama dzinalo.

[C]
Tama dzinalo, Tama dzinalo,
Anandipaka ndi mwaziwo,
Tama dzinalo.

192. Pa Mtanda Pomwe Naferapo

Link copied to clipboard successfully!