Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #189
Hymn 189 Tilibe Mzinda M’dzikoli
[V1]
Tilibe mzinda m’dzikoli
Wolimba, wokhalitsanso;
Komatu tikondwera ’fe,
Tifuna mzinda udzawo,
Tifuna mzinda udzawo.
Tilibe mzinda m’dzikoli
Wolimba, wokhalitsanso;
Komatu tikondwera ’fe,
Tifuna mzinda udzawo,
Tifuna mzinda udzawo.
[V2]
Tilibe mzinda m’dzikoli,
Wolimba, wokhalitsanso;
Tifuna wina m’mwambamo,
Wowala ndi wosathanso,
Wowala ndi wosathanso.
Tilibe mzinda m’dzikoli,
Wolimba, wokhalitsanso;
Tifuna wina m’mwambamo,
Wowala ndi wosathanso,
Wowala ndi wosathanso.
[V3]
Ee, malo a mtenderewo,
Otopawo apumako!
Ndikhala ndi mapikowo,
Ndikadaulukirako,
Ndikadaulukirako.
Ee, malo a mtenderewo,
Otopawo apumako!
Ndikhala ndi mapikowo,
Ndikadaulukirako,
Ndikadaulukirako.
[V4]
Tonthola moyo wanga ’we,
Adziwa nthawi Mlunguyo;
Ndichite ntchito yakeyo,
Apatsa ’ne mpumulowo,
Apatsa ’ne mpumulowo.
Tonthola moyo wanga ’we,
Adziwa nthawi Mlunguyo;
Ndichite ntchito yakeyo,
Apatsa ’ne mpumulowo,
Apatsa ’ne mpumulowo.