Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #170
Hymn 170 Mulungu, Mfumu
[V1]
Mulungu, Mfumu ’Nu, Ndilibe mphamvutu,
Munandilenga, mundisunga Nthawi zonsezi.
Munandilenga, Mundisunga Nthawi zonsezi.

[V2]
Ndilibe winanso, Ndimatsamira ’Nu;
Zabwino zanu zipambana, Ndichitenji ko?
Zabwino zanu zipambana, Ndichitenji ko?
Ndilibe winanso, Ndimatsamira ’Nu;
Zabwino zanu zipambana, Ndichitenji ko?
Zabwino zanu zipambana, Ndichitenji ko?
[V3]
Ndipatse chiyani ko? Poona zonsezi
Zakhala zanu kale ndithu. Ndidzatani ko?

[V4]
Mufuna mtimanga, Ndipatsa msangatu.
Ndikhale wanu nthawi zonse, Mndilandire ’ne.