Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #157
Hymn 157 Wakufetsa Ndi Kulira
[V1]
Wakufesa ndi kulira,
Mbeu za chikondicho,
Wosatopa, wosagona,
Yesu amdalitsa ’ye.
Wakufesa ndi kulira,
Mbeu za chikondicho,
Wosatopa, wosagona,
Yesu amdalitsa ’ye.
[C]
Ona! mmera wakukondwa,
Dzinthu dzonse dzachanso
Ona! m’minda mwayeratu,
Layandika khunkhalo.
Ona! mmera wakukondwa,
Dzinthu dzonse dzachanso
Ona! m’minda mwayeratu,
Layandika khunkhalo.
[V2]
Mvula idzatsirirapo,
Dzuwa ’dzawaliranso,
Ndi zipatso zidzabala,
M’mphamvu ya Mulunguyo.
Mvula idzatsirirapo,
Dzuwa ’dzawaliranso,
Ndi zipatso zidzabala,
M’mphamvu ya Mulunguyo.
[C]
Ona! mmera wakukondwa,
Dzinthu dzonse dzachanso
Ona! m’minda mwayeratu,
Layandika khunkhalo.
Ona! mmera wakukondwa,
Dzinthu dzonse dzachanso
Ona! m’minda mwayeratu,
Layandika khunkhalo.
[V3]
Fesa mbeu, usatope,
Usaope konsetu,
Nkana utapeza vuto,
Udzatuta mokondwa.
Fesa mbeu, usatope,
Usaope konsetu,
Nkana utapeza vuto,
Udzatuta mokondwa.
[C]
Ona! mmera wakukondwa,
Dzinthu dzonse dzachanso
Ona! m’minda mwayeratu,
Layandika khunkhalo.
Ona! mmera wakukondwa,
Dzinthu dzonse dzachanso
Ona! m’minda mwayeratu,
Layandika khunkhalo.