Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #74

Hymn 74 M’mawa Tidzafesa

[V1]
M’mawa tidzafesa mbeu zakukoma,
Msana ndi usiku tidzafesanso,
Nyengo ya masika tidzatema m’munda
Tidzabwera tonse ndi zipatsozo.

[C]
Ndi zipatsozo, ndi zipatsozo
Tidzabwera tonse ndi zipatsozo.

[V2]
Tidzifesa m’dzuwa tidzifesa m’thunzi,
Sitiopa ife mtambo ndi mphepo.
Athatu masika nchitozi zidzatha,
Tidzabwera tonse ndi zipatsozo.

[C]
Ndi zipatsozo, ndi zipatsozo
Tidzabwera tonse ndi zipatsozo.

[V3]
Tingolira kaya koma tidzafesa
Mbeu za Ambuye ntchito ya Yesu.
Adzachotsa msozi adzatilandira,
Tidzabwera tonse ndi zipatsozo.

[C]
Ndi zipatsozo, ndi zipatsozo
Tidzabwera tonse ndi zipatsozo.

74. M’mawa Tidzafesa

Link copied to clipboard successfully!