Back to Khristu Mu Nyimbo List Khristu Mu Nyimbo #132

Hymn 132 Yesu, Mundisungetu

[V1]
Yesu, mundisungetu, Mfupi mtanda wanu;
Ndipezemo kasupe Wondichiza mtima.

[C]
Mtandawo, mtandawo, Nditamanda mtanda,
Mpaka moyo wangawo Udzapume mmwamba.

[V2]
Nsisi zandipezanso, Pomwe pali mtanda.
Ee! Pa mtanda nthandayo Indiunikira.

[C]
Mtandawo, mtandawo, Nditamanda mtanda,
Mpaka moyo wangawo Udzapume mmwamba.

[V3]
Pa mtandapo ndiona Mwana wa Mulungu.
Mndithandize, Mbuyanga, Kuyendabe nanu.

[C]
Mtandawo, mtandawo, Nditamanda mtanda,
Mpaka moyo wangawo Udzapume mmwamba.

[V4]
Pa mtandapo ndzalinda, Ndikuyembekeza,
Mpaka ndidzafika ku Dziko la kumwamba.

[C]
Mtandawo, mtandawo, Nditamanda mtanda,
Mpaka moyo wangawo Udzapume mmwamba.

132. Yesu, Mundisungetu

Link copied to clipboard successfully!