Back to Khristu Mu Nyimbo List
Khristu Mu Nyimbo #120
Hymn 120 Atate, Ndziperekatu
[V1]
Atate, ndziperekatu, Palibe winanso,
Popanda Inu, Mbuyanga, Ndidzanka kutiko?
Atate, ndziperekatu, Palibe winanso,
Popanda Inu, Mbuyanga, Ndidzanka kutiko?
[C]
Eh! Ndikhulupirira ’Ye, Wondifera ine.
Anapereka mwazi ’ke, Kupulumutsa ’ne.
Eh! Ndikhulupirira ’Ye, Wondifera ine.
Anapereka mwazi ’ke, Kupulumutsa ’ne.
[V2]
Ndikhulupira Mwanayo, Ndifuna mphamvu ’ke;
Zoipa zanga zonsezo, Mzichotse Inutu.

[V3]
Kwa Inu, Mbuye, mwini wa Chikhulupirocho,
Mndipatse mphatso yanuyo, Ndingafe m’mtimanga.